" I har fået det for intet, giv det for intet " (Matt 10:8)

HJEM  |  OVERSIGT  |  KONTAKT  |  HJÆLP    
Bibelstudier Gratis Kristne Bøger Gratis Kristne e-Bøger Om Os
 Helt GRATIS Trykte Bøger
- Chichewa udgave # 1

 


Kodi mwabadwadi mwatsopano mwa madzi ndi mwa Mzimu Woyera?

 

Kulengeza:

Ili ndilo buku loyamba mnthawi yathu lakulalika za 'Uthenga wa bwino wa Madzi ndi Mzimu' mogwirizana kwambiri ndi Malembo.

Kufothokoza:

Ndime yamuthu waukhulu ya m'nkhaniyi ndi "ku Badwanso mwa Madzi ndi Mzimu." Muthuyu wachoka mnkhani yomweyi. Kunenetsa, bukuli likufothokoza tanthauzo lakubadwanso ndi mwamene mungabadwirenso mwa madzi ndi Mzimu mogwirizana ndi Bibulo. Madzi akuimirira ubadizo wa Yesu mu Yordani ndipo Babilo likuti machismo athu tonse anaikidwa pa Yesuyo pamene anabadizidwa ndi Yohane Mbatizi. Yohane ankhaimilira anthu amitundu yosina-siyana anali wambanja la Aloni wa Sembe Wamkhulu. Aloniyo aikha manja ake pa mbuzi yopepetsera machimo a Asiraeli achaka chonse Patsiku la Kupepetsera Machismo. Chinali chinthunzi-thunzi cha zinthu zabwino zikubwera. Kubadizidwa kwa Yesu kukufanizira kuikhapo manja kuja. Yesu anabadizidwa m'njira yoikha manja ku mtsinje wa Yordani uja. Ndiye anachotsa machismo adziko lonse paubadizo Wake ndipo anapachikidwa kuti alipe machimo athu. Koma anthu ambiri sakudziwa nchifukwa chanji Yesu anabadizidwa ndi Yohani mu Yordani. Ubadizo wa Yesu ndiyo nfundo yaikhulu mbukuli, imene singasiyanitsidwe ndi Uthenga wa Bwino wa madzi ndi Mzimu. Tingabadwenso ngati tikhulupirira mu ubadizo wa Yesu ndi Mtanda Wake.

Mau a wosindikiza:

Rev. Paul C. Jong wakhala akulalika uthenga wa madzi ndi Mzimu mdziko lonse lapansi kupitirira zaka makumi awiri. Walembanso mithu yankhani yopitirira pa makumi asanu m'mabuku ake ofunika a chi Kristu, Mithu yaikhului yasandulizidwa mzinenero zikhulu-zikhulu zopitirira makumi anai. Mau ake ndi amphamvu ndi uzimu kotere kuti ambiri owerenga mabukuwa anga badwenso ndi kulandira Mzimo Woyera. Tikusimikiza kuti ili ndilo buku loyamba mnthawi yathu lakulalika za Uthenga wa bwino wa madzi ndi Mzimu mogwirizana kwambiri ndi Malembo.


 

 
Free Christian Books
    Trykt Bogliste
    Chichewa udgave 1
 
 • Om denne bog
 •  
 • Indholdsfortegnelse
 •     Om gratisbøger service
      Hvordan bestiller man gratis bøger
      FAQs
  Se
  Kurv
   

     
  Copyright © 2001 - 2019 New Life Mission. Alle rettigheder er forbeholdt.