Search

ΔΩΡΕΑΝ ΤΥΠΩΜΕΝΑ ΒΙΒΛΙΑ,
eBOOKS ΚΑΙ ΒΙΒΛΙΑ ΗΧΟΥ

Η Σκηνή του Μαρτυρίου

CHIHEMA: Chithunzi Chatsatanetsatane cha Yesu Kristu ( II )
  • ISBN8983148527
  • Σελίδες448

Γκα 10

CHIHEMA: Chithunzi Chatsatanetsatane cha Yesu Kristu ( II )

Rev. Paul C. Jong

ZAMKATIMU

Mau Oyamba 
1. Sitili Monga Iwo Amene Abwereranso ku Chionongeko Chifukwa cha Machimo Athu (Yohane 13:1-11) 
2. Nsaru ndi Mizati ya Malo Opatulika (Eksodo 26:31-37) 
3. Iwo Amene Angathe Kulowa m’Malo Opatulikitsa (Eksodo 26:31-33) 
4. Chinsaru Chotchinga Chomwe Chinang’ambika (Mateyu 27:50-53) 
5. Makamwa Awiri Asiliva ndi Mitsukwa Iwiri ya Thabwa Lililonse la Kacisi (Eksodo 26:15-37) 
6. Zinsinsi Zauzimu Zobisidwa mu Likasa la Mboni (Eksodo 25:10-22) 
7. Chopereka cha Chikhululukiro cha Uchimo Choperekedwa pa Chotetezerapo (Eksodo 25:10-22) 
8. Gome la Mkate Woonekera (Eksodo 37:10-16) 
9. Choikapo Nyali cha Golidi (Exodus 25:31-40) 
10. Guwa la Nsembe Lofukizapo (Eksodo 30:1-10) 
11. Mkulu Wansembe Yemwe Ankapereka Chopereka cha Tsiku la Chitetezero (Levitiko 16:1-34) 
12. Zinsinsi Zinai Zobisika mu Zophimba za Chihema (Eksodo 26:1-14) 
13. Ndemanga za Owerenga 
 
Kodi tingapedze motani coonadi co bitsala mu Cihema? Ndi pokhapo podzindikira uthenga wa madzi ndi Mzimu, ceni ceni ca Cihema, ndi pamene tingadziwe yankho ku funso limeneli.
Mcoonadi, nsaru zomwe zitaonekedwa pa kohomo la bwalo la Cihema limatisonyedza zincito za Yesu Kristu mu Cipangano ca Tsopano cimene cidapulumutsa anthu amudziko la pansi. Munjira yotere, Mau a mu Cipangano ca Kale ya mu Cihema ndi Mau a mu Cipangano ca Tsopano yali cimodzimodzi yo fanana, monga nsaru za mu Cihema. Koma, mwatsoka, ici coonadi cankhala cobitsika kwa nthgawi yaitali kwa iwo amene amafuna funa coonadi mu Ukristu.
Pobwera padziko lino, Yesu Kristu anabatizidwa ndi Yohane ndipo ana ketsa mwadzi Wace pa Mtanda. Kopanda kumvetsetsa ndi kukhulupirira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, palibe Umodzi waife yemwe anga dziwe coonadi cobvumbulutsidwa mu Cihema. Tiyenera kudziwa tsopano coonadi ici ca Chihema ndi kukhulupiriramo. Tonsefe tiyenera kudziwa ndi kukhulupirira mu coonadi coonekedwa nsaru zimene zitayalidwa pabwalo ya pakhomo ya Cihema.
Κατεβάστε eBook
PDF EPUB
Βιβλια ηχου
Βιβλια ηχου

Βιβλία που σχετίζονται με αυτόν τον τίτλο

The New Life Mission

Συμμετάσχετε στην έρευνά μας

Πώς μάθατε για εμάς;