Chichewa 5
Choose your preferred file format and safely download to your mobile device, PC, or tablet to read and listen to the sermon collections anytime, anywhere. All eBooks and AudioBooks are completely free.
Mawu a mu bukuli akupha ludzu m,mtima wanu. Akristu a masiku ano akupitiliza kukhala ndi moyo pamene sakudziwa yankho lenileni la machimo enieni amene akuchita tsiku ndi tsiku. Kodi mkuchidziwa chimene n’chilungamo cha Mulungu? Ndikhulupilira kuti mdzazifunsa nokha funsoli ndi kukhulupilira mu chilungamo cha Mulungu, chimene chikuululidwa mu bukuli.
Chilungamo cha Mulungu chakhala ndi uthenga wa madzi ndi Mzimu. Koma, ngati chuma cha mtengo wapatali, chasungidwa mobisika ku maso amene akusatira zazipempbezo kwa nthawi yaitali. Ngati zotulukamo zake, anthu ambiri anadalira pa chimenecho ndi kuzikuza cifukwa cha chilungamo chawo m’malo mwa kukhulupilira mu chilungamo cha Mulungu. Chotero, ziphunzitso za Chikristu zimene si zikupanga ngakhalenso ziganizo zolongosoka zinakhala zikhulupiliro zolamulira m’mitima ya okhulupilira, ngati n’paja ziphunzitsozi zili ndi chilungamo cha Mulungu.
ziphunzitso za Kusankhidwa, Kuyeretsedwa, ndiponso Kusukidwa mwa pang’onopang’ono ndi ziphunzitso zadzikulu za Chikristu, zimene zinabweretsa msokonezo ndi kupanda kanthu m’miyoyo ya okhulupilira. Koma tsopano, Akristu ambiri ayenera kudziwa Mulungu mwatsopano, aphunzire za chilunamo Chake ndipo apitilize kukhala mu chikhulupiliro chosimikizidwa.
"Ambuyathu amene anakhala chilungamo cha Mulungu” adzapatsa moyo wanu kumvetsetsa kwakukulu ndi kuwotsogolera ku mtendere. Mlembi akufuna kuti inu mkhale nalo dalitso la kudziwa chilungamo cha Mulungu. Dalitso la Mulungu likhale nanu!
Although the Covid-19 pandemic has ended, there are still difficulties in sending or receiving our printed books by mail due to various difficult international situations. When the international situation improves and mailing normalizes, we will resume mailing printed books.