Chichewa 6
Choose your preferred file format and safely download to your mobile device, PC, or tablet to read and listen to the sermon collections anytime, anywhere. All eBooks and AudioBooks are completely free.
Chilungamo cha Mulungu chavumbulidwa muuthenga wamadzi ndi Mzimu, umene unakwaniritsidwa ndi kubadizidwa kwa Yesu kuli Yohane ndi mwazi Wake Pamtanda. Tibwerere kuchikhulupiliro cha Chilungamo cha Mulungu, tisachedwe.
Kodi ukudziwa ninji Yesu anabadizidwa ndi Yohne Mbadizi? Ngati Yohane sanabadize Yesu, machismo athu akanapatsidwa kwaiye. Yohane Mbadizi ndiye munthu wamkulu kupambana onse, ndipo ubadizo anapatsa Yesu unalingana ndichifuniro cha Mulungu kuti machismo athu apatsidwe kwa Yesu.
Yesu anabadizidwa kuti asenze machismo a anthu onse papewa pake, ndikufa pamtanda kulipa machismo. Zinthu zonsezi zasintha maganizo anga akuti kubadwanso nciani, chifukwa ndinangodziwa za mwazi pa Mtanda.
Tsopano Mulungu wakupunzitsani kuti Chilungamo chake nhiani kuti tidziwe ndikukhulupilira mu Chilungamo chakecho mwatunthu. Ndithokoza Ambuye chifukwa chamadalitso onsewa.
Although the Covid-19 pandemic has ended, there are still difficulties in sending or receiving our printed books by mail due to various difficult international situations. When the international situation improves and mailing normalizes, we will resume mailing printed books.