" Freely you have received, freely give " (Matthew 10:8)

HOME  |  SITEMAP  |  CONTACT US  |  HELP    
  Free eBook Version of Chichewa edition 7

 


KODI NTHAWI YA WOSUSA KHRISTU, KUPHEDWA KWA AKRISTU, KUKWATULIDWA NDI UFUMU WA ZAKA CHIKWI CHIMODZI IDZABWERA? ( I )

- Ndemanga ndi Ziphunzitso za mu Buku la Chivumbulutso

 • Electronic Book Format : Acrobat PDF Reader
 • Current Downloads : 10
 • About this book
 • Table of Contents
 

Kulengeza

Ndemanga ndi Ziphunzitso za mu Buku la Chivumbulutso.

Kufothokoza

Chitapita chipolowe chazigewenga cha 9/11, mafunso ku “www.raptureready.com” Intaneti saiti pankhani ya nyengo, anachulukira kufika ku mamiliyoni opitilira ku 8 anafika, malinga ndi kafuku-fuku wa CNN ndi TIME, ma Ameleka opitilira pa 59% akhulupilira mkukwatula kosilizira.
Kunena za nyengo, mlembiyu akunena mfundo zeni-zeni za mutu wa buku la Chivumbulutso, kunenanso zakubwera kwa Wosusa Khristu, kuphedwa kwa oyera ndikukwatulidwa kwao, Ufumu wa zaka Chikwi chimodzi, ndi Kumwamba kwa Tsopano ndi Dziko la tsopano-zonse kulingana ndi Malembo wonse ndiponso motsogoleledwa ndi Mzimu Woyera.
Bukuli limapatsa ndemanga za ndime ndi ndime mu Buku la Chuvumbulutso powonjezedwa ndi ziphunzitso zozama za mlembi. Aliyense amene amawerenga bukuli adzadziwa zolinga zonse zimene Mulungu anasungira dzikoli lapansi.
Tsopano ndi nthawi kuti inu mdzindikire chofunikira cheni-cheni mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, kotero kuti mupeze nzeru zimene zingakuomboleni kuchoka ku mayetsero onse ndi masautso a nthawi yamapeto. Ndi mabukuwa awiri, ndiponso pokhulupilira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, mdzakwanitsa kupambana mayetsero onse ndi masautso ananeneredwa mu Chivumbulutso.


Mau a wosindikiza

Mlembi akhala alikulalikra uthenga wa madzi ndi Mzimu ku miyoyo yotaika ya dziko lapansi pafupi-fupi zaka makhumi awiri tsopano.
Okhazikitsa New Life Mission, iye tsopano ali kuphunzitsa ophunzira a Yesu pa Sukulu la New Life Mission.
Atakhazikitsa mipingo yodalilika ya mission, iye akufalitsa uthenga kupyolera mu nchito zake zolemba.
Ma Buku ake tsopano amasulilidwa ndipo akuwerengedwa mzilankhulidwe zopitilira 40 za dziko lapansi.


 
Free Christian eBooks
    eBook List
    Chichewa edition 7
 
 • About this book
 •  
 • Table of Contents
 •     What is eBook?
   
 • About eBook
 •  
 • How to read an eBook?
 •  
 • FAQ
 •  
 • Download Help
 •     eBook Readers
   
 • MS Reader 2.0
 •  
 • Acrobat Reader 4.0
 •  
  Partner's Zone

  register as a coworker
  Bookmark
     
  Copyright © 2001 - 2019 The New Life Mission. All Rights Reserved.