" Kowé padha olèh tanpa nganggo mbayar gunakna tanpa nganggo bayaran " (Matius 10:8)

HOME  |  PETA SITE  |  KONTAK  |  PERTOLONGAN    
Pelajaran Alkitab Buku Kristen Gratis eBook Kristen Gratis Tentang Kami
  E-book gratis dalam bahasa Chichewa edisi 18

 

Chikondi cha Mulungu Chovumbulutsidwa Kupitira mwa Yesu, Mwana Wobadwa Yekha ( I )
- Ziphunzitso pa Uthenga wa Yohane (I)

 • Format e-book : Acrobat PDF Reader
 • Download sampai sekarang : 2
 • Mengenai Buku ini
 • Daftar isi
 

Kulengeza:
Chikondi cha Mulungu Chovumbulutsidwa Kupitira mwa Yesu, Mwana Wobadwa Yekha

Kufothokoza:

Chikodi Chovumbulutsidwa Kupitira mwa Yesu Khristu

Chinalembedwa, “Palibe munthu anaonapo Mulungu ndi kale lonse, Mulungu wobadwa yekha amene ali pachifuwa cha Atate ndiye amene anafotokoza za Mulungu” (Yohane 1:18).
Yesu anaulura mokwana bwanji chikondi cha Mulungu kwaife! Kodi ndi choona cheni-cheni chotani chachipulumutso chili mu uthenga wa madzi ndi Mzimu! Sitinadzitsutse polandira chipulumutso kupitira mu chikhulupiliro chathu mwa Yesu, amene anabwera mwa madzi ndi magazi. (1 Yohane 5:6).
Ndikhulupilira kuti nonsenu m’kukhulupilira mwa Yesu Khristu amene anavumbulutsa chikondi cha Mulungu, sungani chikhulupiliro mu chikondi Chake m’mitima yanu, ndipo nthawi zonse mkhale ndi moyo pacifukwa cha kufalitsa chikondicho. Ndikhulupilira kuti mdzafuna dalitso la chikhulukiro cha uchimo mwa kukumana ndi Mulungu kupitira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu.


Mau a wosindikiza:

Umboni wa mu Baibulo Wakuti Yesu Ananyamura Machimo Onse Adzikoli

Pamene Yesu analandira ubatizo, Iye analamura Yohane M’batizi kuti amubatize Iye, kunena, “Pa nthawi ino lola kuti zikhale choncho, chifukwa n’koyenera kwa ife kutero kuti tikwaniritse chilungamo chonse” (Mateyu 3:15). Ambuye ananyamura machimo onse mwa kulandira ubatizo ndipo anchotsa machimo onsewo mwakuwanyamulira pa Mtanda. Ambuye athu anakwanilitsa chilungamo chonse mwa kunyamura machimo onse adziko kupitira mu ubatizo Wake.
Ichi ndicho cifukwa Yohane M’batizi ananena patsiku losatira la ubatizo wa Yesu, “Taonani! Mwanawankhosa wa Mulungu amene akuchotsa uchimo wa dziko!” (Yohane 1:29) Tiyenera kusunga m’mtima choonadi chakuti si tingalandire chikhululukiro choona cha uchimo kopanda kukhulupilira mu ubatizo Wake limodzi ndi magazi Ake pa Mtanda.

 
Free Christian eBooks
    Daftar e-book
    Edisi bahasa Chichewa 18
 
 • Mengenai Buku ini
 •  
 • Daftar isi
 •     Apakah e-book
   
 • Mengenai e-book
 •  
 • Bagaimana membaca e-book
 •  
 • Pertanyaan yang paling sering ditanyakan
 •  
 • Pertolongan untuk Download
 •     Software pembaca e-book
   
 • MS Reader 2.0
 •  
 • Acrobat Reader 4.0
 •  

     
  Copyright © 2001 - 2019 The New Life Mission. ALL RIGHTS reserved.