Search

БЕЗКОШТОВНІ ЕЛЕКТРОННІ КНИГИ ТА АУДІОКНИГИ

Євангеліє води та Духа

KODI CHOFUNIKIRA NDI CHIANI KWA INU KUTI MUBADWENSO MWATSOPANO?

KODI CHOFUNIKIRA NDI CHIANI KWA INU KUTI MUBADWENSO MWATSOPANO?

Автор Rev. Paul C. Jong ISBN 9788928240876 Сторінки 397
Чичева 65

Завантажте електронні книги та аудіокниги БЕЗКОШТОВНО

📖 Читати онлайн зараз
Майте друковану книгу
Купіть друковану книгу на Amazon

Паперові книги наразі доступні для індивідуальної покупки на Amazon. (Електронні книги Kindle також доступні для завантаження)

Zamkatimu

Mawu Oyamba 
1. Kodi Ndindani Olambira Mumzimu Ndi M’coonadi? (Yohane 4:1-24) 
2. Kodi Zikutanthauza Chiani Kubadwadi Mwatsopano? (Yohane 4:1-19) 
3. Kanani Maganizo Anu (2 Mafumu 5:15-19)
4. Umunthu Wanu Weni Weni Ndi Chikondi Cha Ambuye (Yohane 3:16) 
5. Tiyenera Kubadwa Mwatsopano Pokhulupilira mu Uthenga Wabwino wa Madzi Ndi Mzimu (Yohane 3:1-5)
6. Chikhulupiliro Chomwe Chimagonjetsa Dziko Lino (Yohane 15:1-9) 
7. Kukhulupilira mu Ntchito Ya Mulungu Ndi Kugwira Ntchito Ya Mulungu (Yohane 6:16-29) 
8. Yesu Watsuka Mapazi athu Monga M’mene Anatsukira Mapazi a Petro (Yohane 13:1-11) 
9. Ambuye Wathu Watidalitsa Ife Kuti Titsate Iye Ngakhale Tiri Ndi Zolakwa Zambiri (Yohane 21:15-19)
10. Chofunikira Chenicheni Pogawana Chiyanjano Mwa Kristu (1 Yohane 1-10) 
11. Kodi Zikutanthauza Chiani Pamene Baibulo Lanena Kuti Yense Wakukhala Mwa Mulungu Sachimwa? (1 Yohane 3:1-10) 
12. Kodi Mukufunitsitsadi Kuti Chikhulupiliro Chanu Chikhale Chofanana Monga Chikhulupiliro Cha Petro? (Mateyu 16:13-20) 
13 Chilungamo Cha Ambuye Ndi Chofunika Kotheratu Kwa Ife Amene Timachita Tchimo Nthawi Zonse (Mateyu 9:9-13) 
 
Akristu lero ayenera kusintha maganizo ao. Iwo ayenera kukhulupilira mu Uthenga Wabwino wa madzi ndi Mzimu woperekedwa ndi Mulungu monga chipulumutso chao cheni cheni. Tonse tiyenera kuthokoza Ambuye potipatsa ife Uthenga umenewu Wabwino wa madzi ndi Mzimu. Kodi m’malo mwake tinganene bwanji kuti ntchito ya Ambuye ya chipulumutso yomwe yaombola ife ku machimo onse a dziko kuti ndiyolakwika? Kudzera m’bukuli pa Uthenga Wabwino wa madzi ndi Mzimu, ali yense tsopano ayenera kubadwa mwatsopano pokhulupilira muchipulumutso chomwe Ambuye wakwaniritsa kamodzi kokha. Ngati simukutsimikizabe za izi, muyenera kachiwiri kusinkhasinkha mwakuya pa chilungamo cha Mulungu chomwe Ambuye wapereka kwa inu.
Більше