Search

免费印刷书籍、
电子书和有声读物

会幕

奇切瓦语 9

CHIHEMA: Chithunzi Chatsatanetsatane cha Yesu Kristu ( I )

Rev. Paul C. Jong | ISBN 9788928231843 | 页码 378

下载免费电子书和有声读物

选择您喜欢的文件格式,安全下载到手机、电脑或平板电脑,随时随地阅读和收听讲道集。所有电子书和有声读物都完全免费。

您可以通过下方播放器收听有声读物。🔻
拥有平装书
在亚马逊购买平装书
ZAMKATIMU
 
Mau Oyamba 

1. Chipulumutso cha Ochimwa Choonetsedwa mu Chihema (Eksodo 27:9-21) 
2. Ambuye Wathu Yemwe Anabvutika Chifukwa cha Ife (Yesaya 52:13-53:9) 
3. Yawe Mulungu Wamoyo (Eksodo 34:1-8) 
4. Chifukwa Chimene Mulungu Anaitanira Mose ku Phiri la Sinai (Eksodo 19:1-6) 
5. M’mene Aisrayeli Ankaperekera Nsembe mu Chihema: Mbiri Yoyamba (Genesis 15:1-21) 
6. Lonjezo La Mulungu Lokhazikitsidwa mu Pangano Lake la Mdulidwe Lidakali ndi Ntchito kwa Ife (Genesis 17:1-14) 
7. Zipangizo Zomangira Chihema Zomwe Zinaika Maziko a Chikhulupiliro (Eksodo 25:1-9) 
8. Mtundu wa Chipata cha Bwalo la Chihema (Eksodo 27:9-19) 
9. Chikhulupiliro Choonetsedwa mu Guwa la Nsembe (Exodus 27:1-8) 
10. Chikhulupiliro Choonetsedwa mu Mkhate Wosambiramo (Eksodo 30:17-21) 
11. Umboni wa Chipulumutso 
 
Kodi tingapedze motani coonadi co bitsala mu Cihema? Ndi pokhapo podzindikira uthenga wa madzi ndi Mzimu, ceni ceni ca Cihema, ndi pamene tingadziwe yankho ku funso limeneli.
Mcoonadi, nsaru zomwe zitaonekedwa pa kohomo la bwalo la Cihema limatisonyedza zincito za Yesu Kristu mu Cipangano ca Tsopano cimene cidapulumutsa anthu amudziko la pansi. Munjira yotere, Mau a mu Cipangano ca Kale ya mu Cihema ndi Mau a mu Cipangano ca Tsopano yali cimodzimodzi yo fanana, monga nsaru za mu Cihema. Koma, mwatsoka, ici coonadi cankhala cobitsika kwa nthgawi yaitali kwa iwo amene amafuna funa coonadi mu Ukristu.
Pobwera padziko lino, Yesu Kristu anabatizidwa ndi Yohane ndipo ana ketsa mwadzi Wace pa Mtanda. Kopanda kumvetsetsa ndi kukhulupirira mu uthenga wa madzi ndi Mzimu, palibe Umodzi waife yemwe anga dziwe coonadi cobvumbulutsidwa mu Cihema. Tiyenera kudziwa tsopano coonadi ici ca Chihema ndi kukhulupiriramo. Tonsefe tiyenera kudziwa ndi kukhulupirira mu coonadi coonekedwa nsaru zimene zitayalidwa pabwalo ya pakhomo ya Cihema.
更多
有声书播放器

与该标题相关的书籍

The New Life Mission

参加我们的调查

您是如何了解到我们的?