Search

免費印刷書籍、
電子書和有聲讀物

聖靈

奇切瓦語 3

Mzimu Woyera Amene Amakhala mwa Ine - Njira-yabwino kwa Inu Kuti Mulandire Mzimu Woyera

Rev. Paul C. Jong | ISBN 8983141069 | 頁碼 361

下載免費電子書和有聲讀物

選擇您喜歡的文件格式,安全下載到手機、電腦或平板電腦,隨時隨地閱讀和收聽講道集。所有電子書和有聲讀物都完全免費。

您可以通過下方播放器收聽有聲讀物。🔻
擁有平裝書
在亞馬遜購買平裝書
ZAMKATIMU

Mau Oyamba

Gawo Loyamba – Ulaliki
1. Mzimu Woyera Umagwira Ntchito Mkati mwa Mawu a Mulungu a Lonjezo (Macitidwe a Atumwi 1:4-8) 
2. Kodi WinaWake Angathedi Kugula Mzimu Woyera Mwa Kulimbikila Kwake? (Macitidwe a Atumwi 8:14-24) 
3. Kodi Munalandira Mzimu Woyera Pamene Munakhulupilira mwa Yesu? (Macitidwe a Atumwi 19:1-3) 
4. Iwo Amene ali ndi Chikhulupiliro Chofanana Monga cha Ophunzira a Yesu (Macitidwe a Atumwi 3:19) 
5. Kodi Mukufuna Kukhala Muchiyanjano ndi Mzimu Woyera? (1 Yohane 1:1-10) 
6. Khulupilirani Kuti Mzimu Woyera Umakhala mwa Inu (Mateyu 25:1-12) 
7. Uthenga Wabwino Okoma Umene Umakulolani inu Kuti Mzimu Woyera Ukhale mu Mtima Wanu (Yesaya 9:6-7) 
8. Kodi ndi Kudzera Mwa Ndani M’mene Madzi Amoyo a Mzimu Woyera Amayenda? (Yohane 7:37-38) 
9. Uthenga Wabwino wa Ubatizo wa Yesu Umene Watipanga Ife Kukhala Oyera (Aefeso 2:14-22) 
10. Yendani mu Mzimu! (Agalatiya 5:16-26, 6:6-18) 
11. Kusunga Moyo Wanu Odzala ndi Mzimu Woyera (Aefeso 5:6-18) 
12. Kukhala Moyo Wanu Odzala ndi Mzimu Woyera (Tito 3:1-8) 
13. Ntchito ndi Mphatso za Mzimu Woyera (Yohane 16:5-11) 
14. Kodi Kulapa Koona Kumene Kumatitsogolera Ife Kuti Tilandire Mzimu Woyera ndi Kotani? (Macitidwe a Atumwi 2:38) 
15. Mungalandire Mzimu Woyera Ndi Kukhala Naye Pokhapo Ngati Mwadziwa Choonadi (Yohane 8:31-36) 
16. Ntchito ya Onse Amene Alandira Mzimu Woyera (Yesaya 61:1-11) 
17. Tiyenera Kukhala ndi Chikhulupiliro Komanso Chiyembekezo mu Mzimu Woyera (Aroma 8:16-25) 
18. Choonadi Chimene Chimakutsogolerani Inu ku Kukhazikika kwa Mzimu Woyera (Yoswa 4:23) 
19. Uthenga Wabwino Okoma Umene Unang’amba Nsaru Yotchinga Mkachisi (Mateyu 27:45-54) 
20. Iwo Amene Anadziwa Kukhazikika Kwa Mzimu Woyera Amatsogolera Ena Kuti Alandirenso Mzimu Woyera (Yohane 20:21-23) 

Gawo Lachiwiri-Zowonjezera
1. Umboni wa Chipulumutso 
2. Mafunso ndi Mayankho 
 
Mchikristu cha masiku ano, nkhani zokambilana zambiri ndi “chipulutso ku uchimo” ndi “kukhala kwa Mzimu Woyera.” Koma, ndi anthu ochepa amene ali ndi nzeru yeniyeni ya mfundo ziwirizi, ngakhale choona ndi chakuti zinthu ziwiri n’zofunikira mfundo za Chikristu. Chimene chikuoopsa kwambiri, sitingapeza cholemba cha mu baibulo chilichonse chimene chikutiphunzitsa molondola za nkhani za pamwambapa. Kunali alembic ambiri a zachikristu kulemekeza mphatso za Mzimu Woyera kapena kufotokoza miyoyo yodzadza ndi Mzimu. Koma palibe wina aliyense wa iwo amene akuyetsa kuthana ndi funso lenileni, “Kodi okhulupilira angalandiredi motani Mzimu Woyera?” Kodi chifukwa n’chiyani? Choonadi chodabwitsa ndi chakuti sanalembepo za ichi mozama chifukwa alibe nzeru yeniyeni ya zachimenechi. Monga m’mene Mneneri Hoseya anafuura, “Anthu anga akuonongeka chifukwa akusowa nzeru,” masiku ano, palibe ngakhale Akristu ochepa amene sakutengedwera mu chipembezo chotentheka, kuyembekezera kulandira Mzimu Woyera. Iwo akukhulupira kuti adzalandira Mzimu Woyera mwa kufika pakaonekedwe kakufunitsitsa ndi kamisala. Koma sikulongola kunena kuti chotchedwa chikhulupiliro chawo chikubwezera Chikristu mu matsenga wamba, ndi kuti kutentheka kotere kukuchokera kwa Satana. Mlembi Rev. Paul C. Jong akufuna kulengeza choonadi. Iye akuthana ndi mutu ofunikira mozama, umene alembe ambiri auzimu auzemba kwa nthawi yaitali. Iye poyamba akumasulira tanthauzo la “kubadwa mwatsopano” ndi “kukhala kwa Mzimu Woyera,” ndipo akumasulira mgiwirizona osaleketsedwa pakati pa mfundo zapakati ziwirizi. Kenako iye akutsogolera ndondomeko yonse ya kufotokoza kokhuzana ndi Mzimu Woyera, kuyambira, “m’mene mngadziwire mizimu,” mpaka “kunjira ya miyoyo yodzala ndi Mzimu.” Kuti mdziwe zambiri , mlembi akukulimbikitsani kuti muyeze zamkati mwa bukuli loikidwa pa webisaitiyi.
更多
有聲書播放器

與該標題相關的書籍

The New Life Mission

參加我們的調查

您是如何得知我們的?