Search

免費印刷書籍、
電子書和有聲讀物

水與靈的福音

奇切瓦語 53

NZERU YA UTHENGA WABWINO WAKALE

Rev. Paul C. Jong | ISBN 9788928240777 | 頁碼 422

下載免費電子書和有聲讀物

選擇您喜歡的文件格式,安全下載到手機、電腦或平板電腦,隨時隨地閱讀和收聽講道集。所有電子書和有聲讀物都完全免費。

您可以通過下方播放器收聽有聲讀物。🔻
擁有平裝書
在亞馬遜購買平裝書
Zamkatimu

Mawu Oyamba 

1. Kodi Tchimo Loyamba la Anthu Ndi Chiani? (Marko 7:20-23) 
2. Kodi Uthenga Wabwino Unakwaniritsidwa ndi Mwazi Okha, kapena ndi Madzi, kapena ndi Zonse? (Eksodo 12:43-49) 
3. Ubwenzi Pakati Pa Utumiki Wa Yohane Mbatizi Ndi Uthenga Wabwino Wa Chitetezero Cha Machimo (Mateyu 21:32) 
4. Kodi Tanthauzo Leni Leni La kubadwanso Mwatsopano Ndi Chiani? (Yohane 3:1-15) 
5. Nsembe Yonsinthidwa (Ahebri 7:1-28)
6. Mwanawankhosa wa Mulungu Amene Achotsa Tchimo Lache La dziko Lapansi! (Yohane 1:29) 
7. Uthenga Wabwino Wa Chitetezero Omwe Wafufuta Machimo Anu Onse a Masiku Onse (Yohane 13:1-17)
8. Uthenga Wabwino Wakale Omwe Ungagonjetse Machimo a Dziko Lapansi (1 Yohane 5:4-9) 
 
Uthenga Wabwino wakale otchulidwa m’buku ili ndi Uthenga Wabwino oyamba otchedwa kuti “Uthenga Wabwino wa madzi ndi Mzimu.” Mpaka pano, komabe, Akristu ambiri sakudziwa kuti Uthenga Wabwino wa madzi ndi Mzimu ndiye Uthenga Wabwino oyamba, ndipo zotsatira zake akhulupilira molakwika mu ‘Uthenga wa hafu’. Ndi chifukwa chake chikhulupiliro chao sichipita patali, ndipo zakhala zosatheka kwa iwo kuona kukula mu uzimu. Chikhulupiliro chao chakhala choperewera nthawi zonse, chodzadza ndi malamulo kapena chikhulupiliro cha zinsinsi. Zotsatira zake sangadzithandize okha koma kukhala ndi mitima yochimwa. Kodi ndi mphamvu yanji ya uzimu yomwe Akristu otere angakhale nayo pamene adakali ndi machimo m’mitima yao? Chifukwa akhala Akristu opanda mphamvu, myoyo yao mu dziko lino ilibenso ntchito. Tinganene tsopano kuti Akristu alero ali ndi Uthenga wa hafu kuyambira pa nthawi yomwe mpingo oyamba unatha. Motero, tonse a ife tiyenera kuzindikiranso Uthenga Wabwino wakale tsopano nthawi isanathe, dziwani chikondi cha Mulungu choonadi ndi kukhulupilira mu chikondi choonadichi.
更多

與該標題相關的書籍

The New Life Mission

參加我們的調查

您是如何得知我們的?